
Tikukonza, mabizinezi 27 adzipanga a Malawi okhaokha – Mumba
Nzika za mayiko ena zomwe zili mdziko muno ndipo zikupanga mabizinezi ang’onoang’ono, zikuyenera kupeza zina zochita pomwe boma kudzera ku unduna wa zamalonda lalengeza kuti likumalizitsa lamulo loletsa nzika za mayiko enazi kupanga bizinezi komaso kugwira …